Yohane 10:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yesu anayankha iwo, Ndakuuzani, ndipo simukhulupirira, Nchitozi ndizicita Ine m'dzina la Atate wanga, zimenezi zindicitira umboni.

Yohane 10

Yohane 10:19-26