Yobu 8:14-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Kulimbika mtima kwace kudzatyoka,Cikhulupiriro cace cikunga nyumba ya tandaude.

15. Adzatsamira nyumba yace, koma yosamlimbira;Adzaiumirira koma yosakhalitsa.

16. Akhala wamuwisi pali dzuwa,Ndi nthambi zace ziturukira pamunda pace.

Yobu 8