Yobu 8:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo anayankha Bilidadi Msuki, nati,

2. Udzanena izi kufikira liti?Ndipo mau a pakamwa pako adzakhala ngati namondwe kufikira liti?

3. Ngati Mulungu akhotetsa ciweruzo?Ngati Wamphamvuyonse akhotetsa mlandu?

4. Cinkana ana ako anamcimwira Iye,Ndipo anawapereka mwa kulakwa kwao;

Yobu 8