Yobu 6:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mibvi ya Wamphamvuyonse yandilowa,Mzimu wanga uumwa ulembe wace;Zoopsa za Mulungu zindindandira nkhondo.

Yobu 6

Yobu 6:1-10