Yobu 6:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma Yobu anayankha, nati,

2. Mwenzi atayesa bwino cisoni canga,Ndi kuika matsoka anga pamodzi pamuyeso!

3. Pakuti zikadalemera tsopano koposa mcenga wa kunyanja;Cifukwa cace mau anga ndasonthokera kunena.

Yobu 6