Yobu 41:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Kodi ukhoza kukoka ng'ona ndi mbedza?Kapena kukanikiza kalandira wace ndi cingwe?

2. Kodi ukhoza kumanga m'mphuno ndi mlulu?Kapena kuboola nsagwada wace ndi momba?

3. Kodi idzacurukitsa mau akukupembedza?Kapena idzanena nawe mau ofatsa?

4. Kodi idzapangana ndi iwe,Kuti uitenge ikhale kapolo wako wacikhalire?

Yobu 41