Yobu 4:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo Elifazi wa ku Temani anayankha, nati,

2. Munthu akayesa kunena nawe mau, kodi udzamva nao cisoni?Koma akhoza ndani kudziletsa kunena?

Yobu 4