Yobu 39:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Kodi udziwa nyengo yakuswana zinkhoma?Kodi wapenyerera pakuswa nswala?

2. Ukhoza kodi kuwerenga miyezi yakuzipitira,Kapena udziwa nyengo yoti ziswane?

3. Zithuntha, ziswa,Zitaya zowawa zao.

Yobu 39