Yobu 38:39-40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

39. Kodi ukhoza kusakira mkango waukazi nyama?Ndi kukwaniritsa cakudya ca misona,

40. Pamene ibwathama m'ngaka mwao,Nikhala mobisala kulaliramo?

Yobu 38