Yobu 37:9-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. M'cipinda mwace muturuka kabvumvulu,Ndi cisanu cifuma kumpoto.

10. Mwa kupuma kwace apereka cipale,Ndi madzi acitando aundana.

11. Asenzetsanso mtambo wakuda bii madzi,Afunyulula mtambo wokhalamo mphezi yace;

Yobu 37