Yobu 37:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo utembenuka-tembenuka pakulangiza kwace,Kuti ucite ziri zonse aulamulira,Pa nkhope ya dziko lokhalamo anthu;

Yobu 37

Yobu 37:6-15