Yobu 37:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pa icinso mtima wanga unienjemera,Nusunthika m'malo mwace.

2. Mvetsetsani cibumo ca mau ace,Ndi kugunda koturuka m'kamwa mwace.

3. Akumveketsa pansi pa thambo ponse,Nang'anipitsa mphezi yace ku malekezero a dziko lapansi.

Yobu 37