Yobu 36:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Elihu nabwereza, nati,

2. Mundilole pang'ono, ndidzakuuzani,Pakuti ndiri naonso mau akunenera Mulungu.

3. Ndidzatenga nzeru zanga kutali,Ndidzabvomereza kuti Mlengi wanga ndi wolungama.

Yobu 36