Yobu 33:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Komatu, Yobu, mumvere maneno anga,Mucherere khutu mau anga.

2. Taonani tsono, ndatsegula pakamwa panga,Lilime langa lanena m'kamwa mwanga.

Yobu 33