Yobu 30:3-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Atsala mafupa okha okha ndi kusowa ndi njala;Akungudza nthaka youma kuli mdima wa m'cipululu copasuka.

4. Achera terere lokolera kuzitsamba,Ndi cakudya cao ndico mizu ya dinde.

5. Anawapitikitsa pakati pa anthu,Awapfuulira ngati kutsata mbala.

6. Azikhala m'zigwa za cizirezire,M'maenje a m'nthaka ndi m'mapanga.

Yobu 30