Yobu 3:23-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. Amuonetseranji kuunika munthu wa njira yobisika,Amene wamtsekera Mulungu?

24. Pakuti ndikati ndidye, kumadza kuusa moyo kwanga;Ndi kudzuma kwanga kumathiridwa ngati madzi.

25. Pakuti cimene ndinaciopa candigwera,Ndi cimene ndacita naco mantha candidzera.

26. Wosakhazikika, ndi wosakhala cete, ndi wosapumula ine,Koma mabvuto anandidzera.

Yobu 3