Yobu 3:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Atatero, Yobu anatsegula pakamwa pace, natemberera tsiku lace. Nalankhula Yobu nati,