Yobu 28:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma kuli mtapo wa siliva, Ndi malo a golidi amene amuyenga.

2. Citsulo acitenga m'nthaka,Ndi mkuwa ausungunula kumwala.

3. Munthu athawitsa mdima,Nafunafuna mpaka malekezero onse,Miyala ya mdima wa bii ndi ya mthunzi wa imfa.

Yobu 28