Yobu 27:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Yobu anaonjezanso mwambi wace, nati,

2. Pali Mulungu, amene anandicotsera zoyenera ine,Ndi Wamphamvuyonse, amene anawawitsa moyo wanga,

3. Pakuti moyo wanga wonse ukali mwa ine,Ndi mpweya wa Mulungu m'mphuno mwanga;

Yobu 27