Yobu 26:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma Yobu anayankha, nati,

2. Wamthandiza bwanji wopanda mphamvu,Kulipulumutsa dzanja losalimba!

3. Wampangira bwanji wopanda nzeruyu!Ndi kudziwitsa nzeru zeni zeni mocurukal

4. Wafotokozera yani mau?Ndi mzimu wa yani unaturuka mwa iwe?

Yobu 26