Yobu 25:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Pamenepo Bilidadi wa ku Suki anayankha, nati, Kulamulira ndi kuopsa kuti ndi Iye;Acita mtendere pa zam'mwamba zace.