Yobu 25:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo Bilidadi wa ku Suki anayankha, nati,

2. Kulamulira ndi kuopsa kuti ndi Iye;Acita mtendere pa zam'mwamba zace.

Yobu 25