Yobu 23:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Koma Yobu anayankha, nati, Lero lomwe kudandaula kwanga kumawawa;Kulanga kwanga kuposa kubuula kwanga m'kulemera