Yobu 22:10-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10. Cifukwa cace misampha ikuzinga.Ndi mantha akubvuta modzidzimutsa,

11. Kapena mdima kuti ungaone,Ndi madzi aunyinji akumiza.

12. Kodi Mulungu sakhala m'mwamba m'tali?Ndipo penyani kutalika kwace kwa nyenyezi, ziri m'talitali.

13. Ndipo ukuti, Adziwa ciani Mulungu?Aweruza kodi mwa mdima wa bii?

Yobu 22