Yobu 21:10-14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10. Ng'ombe yao yamphongo imakwera, yosakanika;Ng'ombe yao yaikazi imaswa, yosapoloza.

11. Aturutsa makanda ao ngati gulu,Ndi ana ao amabvinabvina.

12. Ayimbira lingaka ndi zeze,Nakondwera pomveka citoliro.

13. Atsekereza masiku ao ndi zokoma,Natsikira m'kamphindi kumanda.

14. Koma adati kwa Mulungu, Ticokereni;Pakuti sitifuna kudziwa njira zanu.

Yobu 21