Yobu 2:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pokweza maso ao ali kutali, sanamdziwa, nakweza mau ao, nalira; nang'amba yense maraya ace, nawaza pfumbi kumwamba ligwe pamitu pao.

Yobu 2

Yobu 2:2-13