Yobu 2:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ananena naye, Ulankhula monga amalankhula akazi opusa. Ha! tidzalandira zokoma kwa Mulungu kodi, osalandiranso zoipa? pa ici conse Yobu sanacimwa ndi milomo yace.

Yobu 2

Yobu 2:7-13