Yobu 19:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma Yobu anayankha, nati,

2. Mudzasautsa moyo wanga kufikira liti,Ndi kundityolatyola nao mau?

3. Kakumi aka mwandicititsa manyazi;Mulibe manyazi kuti mundiumira mtima.

Yobu 19