Yobu 17:12-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Zisanduliza usiku ukhale usana;Kuunika kuyandikana ndi mdima.

13. Ndikayembekezera kumanda kukhale nyumba yanga;Ndikayala pogona panga mumdima.

14. Ndikati kwa dzenje, Ndiwe atate wanga;Kwa mphutsi, Ndiwe mai wanga ndi mlongo wanga;

15. Ciri kuti ciyembekezo canga?Inde, ciyembekezo canga adzaciona ndani?

Yobu 17