Yobu 17:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mzimu wanga watha, masiku anga afafanizika,Kumanda kwandikonzekeratu.

2. Zoonadi, ali nane ondiseka;Ndi diso langa liri cipenyere m'kundiwindula kwao.

Yobu 17