Yobu 13:6-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. Tamvani tsono kudzikanira kwanga,Tamverani kudzinenera kwa milomo yanga.

7. Kodi munenera Mulungu mosalungama,Ndi kumnenera Iye monyenga?

8. Kodi mukhalira kumodzi ndi Iye?Mundilimbirana mwa Mulungu.

9. Ncokoma kodi kuti Iye akusanthuleni?Kodi mudzamnyenga Iye monga munyenga munthu?

10. Adzakudzudzulani ndithu,Mukacita tsankhu m'tseri.

Yobu 13