Yobu 13:10-12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10. Adzakudzudzulani ndithu,Mukacita tsankhu m'tseri.

11. Ukulu wace sukucititsani mantha,Ndi kuopsa kwace sikukugwerani kodi?

12. Zikumbutso zanu ndizo miyambi ya mapulusa;Zodzikanira zanu zikunga malinga adothi.

Yobu 13