Yobu 13:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Taonani; diso langa laciona conseci;M'khutu mwanga ndacimva ndi kucizindikira.

2. Cimene mucidziwa inu, inenso ndicidziwa;Sindikuceperani.

3. Koma ine ndidzanena ndi Wamphamvuyonse,Ndipo ndifuna kudzikanira kwa Mulungu.

Yobu 13