Yobu 12:19-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Apita nao, ansembe atawafunkhica,Nagubuduza amphamvu.

20. Amcotsera wokhulupirika kunena kwace.Nalanda luntha la akulu.

21. Atsanulira mnyozo pa akalonga,Nawasezera olimba lamba lao.

22. Abvumbulutsa zozama mumdima,Naturutsa mthunzi wa imfa ukhale poyera;

Yobu 12