Yobu 1:21-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. nati, Ndinaturuka m'mimba ya mai wanga wamarisece, wamarisece ndidzanrukanso; Yehova anapatsa, Yehova watenga, lidalitsike dzina la Yehova.

22. Mwa ici conse Yobu sanacimwa, kapena kunenera Mulungu colakwa.

Yobu 1