Yobu 1:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akali cilankhulire uyu, anadza winanso, nati, Wagwa moto wa Mulungu wocokera kumwamba, wapsereza nkhosa ndi anyamata, nuzinyeketsa; ndipo ndapulumuka ine ndekha kudzakuuzani.

Yobu 1

Yobu 1:11-21