Yesaya 9:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Manase adzadya Efraimu ndi Efraimu adzadya Manase, ndipo iwo pamodzi adzadyana ndi Yuda. Mwa izi zonse mkwiyo wace sunacoke, koma dzanja lace liri citambasulire.

Yesaya 9

Yesaya 9:18-21