Yesaya 8:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Citani phokoso, anthu inu, koma mudzatyokatyoka; cherani khutu, inu nonse a maiko akutari; kwindani nokha, koma mudzatyokatyoka; kwindani nokha, koma mudzatyokatyoka.

Yesaya 8

Yesaya 8:6-11