Yesaya 8:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa kuti mwana asakhale ndi nzeru yakupfuula, Atate wanga, ndi Amai wanga, cuma ca Damasiko ndi cofunkha ca Samariya cidzalandidwa pamaso pa mfumu ya Asuri.

Yesaya 8

Yesaya 8:1-8