Yesaya 7:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mutu wa Aramu ndi Damasiko, ndi mutu wa Damasiko ndi Rezini, zisadapite zaka makumi asanu ndi limodzi mphambu zisanu Efraimu adzatyokatyoka, sadzakhalanso mtundu wa anthu;

Yesaya 7

Yesaya 7:1-10