Yesaya 7:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anauza a nyumba ya Davide, kuti Aramu wapangana ndi Efraimu. Ndipo mtima wace unagwedezeka, ndi mtima wa anthu ace, monga mitengo ya m'nkhalango igwedezeka ndi mphepo.

Yesaya 7

Yesaya 7:1-5