Yesaya 7:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala tsiku limenelo kuti Yehova adzayimbira mluzu cimphanga ciri m'mbali ya kumtunda kwa nyanja za Aigupto, ndi njuci iri m'dziko la Asuri.

Yesaya 7

Yesaya 7:15-23