Yesaya 7:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Ambuye mwini yekha adzakupatsani inu cizindikilo; taonani namwali adzaima, nadzabala mwana wamwamuna, nadzamucha dzina lace Imanueli.

Yesaya 7

Yesaya 7:13-23