Yesaya 65:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

amene akhala pakati pa manda, ndi kugona m'malo am'tseri; amene adya nyama ya nkhumba, ndi msuzi wa zinthu zonyansa uli m'mbale zao;

Yesaya 65

Yesaya 65:1-8