Yesaya 65:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndatambasulira manja anga tsiku lonse kwa anthu opanduka, amene ayenda m'njira mosati mwabwino, kutsata maganizo ao ao;

Yesaya 65

Yesaya 65:1-5