Yesaya 65:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzasangalala m'Yerusalemu, ndi kukondwera mwa anthu anga; ndipo mau akulira sadzamvekanso mwa iye, pena mau akupfuula.

Yesaya 65

Yesaya 65:9-25