Yesaya 65:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma inu amene mwasiya Yehova, amene mwaiwala phiri langa lopatulika, ndi kukonzera mlungu wamwai gome, ndi kudzazira mlungu waimfa zikho za vinyo wosanganiza;

Yesaya 65

Yesaya 65:7-12