Yesaya 63:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti anati, Zoonadi iwo ndiwo anthu anga, ana amene sangacite monyenga; comweco Iye anali Mpulumutsi wao.

Yesaya 63

Yesaya 63:1-11