Yesaya 63:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tayang'anani kunsi, taonani pokhala panu poyera, ndi pa ulemerero wanu, cangu canu ndi nchito zanu zamphamvu ziri kuti? mwanditsekerezera zofunafuna za mtima wanu ndi cisoni canu.

Yesaya 63

Yesaya 63:10-19