Yesaya 63:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iwo anapandukira ndi kumvetsa cisoni mzimu wace woyera, cifukwa cace Iye anasandulika mdani wao, nawathira nkhondo Iye yekha.

Yesaya 63

Yesaya 63:5-14